Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyi mʼpamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndi amene ayenera kunyamula Likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula Likasa la Yehova ndiponso azimutumikira nthawi zonse.”+

  • 1 Mbiri 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Alevi anakanyamula Likasa la Mulungu woona pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo,+ mogwirizana ndi zimene Mose anawalamula potsatira mawu a Yehova.

  • 2 Mbiri 5:4-6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera ndipo Alevi ananyamula Likasa.+ 5 Iwo ananyamula Likasa, chihema chokumanako+ ndiponso ziwiya zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi* anabweretsa zinthuzi. 6 Mfumu Solomo ndi gulu lonse la Aisiraeli amene anawaitana, anasonkhana patsogolo pa Likasa. Iwo anapereka nsembe+ zosawerengeka za nkhosa ndi ngʼombe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena