Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mfumu inkakhala mʼnyumba yake*+ ndipo Yehova anachititsa kuti izikhala mwamtendere komanso isamavutitsidwe ndi adani ake onse. 2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+ 3 Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene mtima wanu ukufuna, chifukwa Yehova ali nanu.”+

  • 1 Mbiri 17:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Davide atangoyamba kukhala mʼnyumba* yake, anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la pangano la Yehova likukhala mutenti.”+ 2 Natani anauza Davide kuti: “Chitani chilichonse chimene mtima wanu ukufuna, chifukwa Mulungu woona ali nanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena