-
1 Mbiri 28:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo pa ana anga onse (poti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.+
6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+
-