Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 7:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikatseka kumwamba ndipo mvula sinagwe, ndikalamula dzombe kuti lidye zomera zamʼdzikoli, ndikatumiza mliri pakati pa anthu anga, 14 anthu anga otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa,+ kupemphera, kundifunafuna komanso kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba nʼkuwakhululukira tchimo lawo ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+

  • Danieli 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena