Salimo 106:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Ndi kutisonkhanitsa pamodzi kuchokera mʼmitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,Komanso kuti tikutamandeni mosangalala.+
47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Ndi kutisonkhanitsa pamodzi kuchokera mʼmitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,Komanso kuti tikutamandeni mosangalala.+