2 Mbiri 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lakopa.*+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.
4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lakopa.*+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.