Levitiko 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzawononga malo anu opatulika olambirirako+ ndipo ndidzagwetsa maguwa anu ofukizirapo zonunkhira. Ndidzaunjika mitembo yanu pamwamba pa mafano anu onyansa* opanda moyowo,+ ndipo ndidzachoka pakati panu monyansidwa.+ Deuteronomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+
30 Ndidzawononga malo anu opatulika olambirirako+ ndipo ndidzagwetsa maguwa anu ofukizirapo zonunkhira. Ndidzaunjika mitembo yanu pamwamba pa mafano anu onyansa* opanda moyowo,+ ndipo ndidzachoka pakati panu monyansidwa.+
5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+