13Mʼchaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira kwa zaka 17.
23 Mʼchaka cha 15 cha Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, Yerobowamu+ mwana wa Yehoasi mfumu ya Isiraeli anakhala mfumu ku Samariya ndipo analamulira zaka 41.