-
2 Mbiri 26:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Nkhani zina zokhudza Uziya, kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi. 23 Kenako Uziya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake, koma anamuika kunja kwa manda a mafumu chifukwa anati: “Ndi wakhate.” Ndiyeno mwana wake Yotamu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
-