Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:28-30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mfumuyo itakambirana ndi anthu ena inapanga ana awiri a ngʼombe agolide,+ kenako inauza anthu onse kuti: “Ndikuona kuti mukuvutika kwambiri kupita ku Yerusalemu. Ndiye ndakupangirani Mulungu uyu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo+ Aisiraeli inu.” 29 Choncho mwana wa ngʼombe wina anamuika ku Beteli+ ndipo wina anakamuika ku Dani.+ 30 Zimenezi zinachititsa kuti anthuwo achimwe+ ndipo iwo ankakafika mpaka ku Dani kukalambira mwana wa ngʼombeyo.

  • 1 Mafumu 13:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ngakhale kuti zimenezi zinachitika, Yerobowamu sanasiye kuchita zoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kuti akhale ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye ankamʼpatsa ponena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”+

  • 1 Mafumu 14:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye adzasiya Aisiraeli chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita ndiponso amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iyeyo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena