1 Mbiri 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene amakhala pali ulemu ndi ulemerero,+Pokhala pake pali mphamvu ndi chimwemwe.+ Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+