1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndikupatsa zimene wapempha.+ Ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ kuposa anthu onse amene anakhalapo mʼmbuyomu komanso amene adzakhaleko mʼtsogolo.+ 2 Mbiri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ufumu wa Solomo mwana wa Davide unakhala wamphamvu. Yehova Mulungu wake anali naye ndipo anamuchititsa kukhala wamphamvu kwambiri.+ 2 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndikupatsa nzeru ndi luso lodziwa zinthu. Ndikupatsanso katundu, chuma ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhaleko ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+ Mlaliki 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.
12 ndikupatsa zimene wapempha.+ Ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ kuposa anthu onse amene anakhalapo mʼmbuyomu komanso amene adzakhaleko mʼtsogolo.+
1 Ufumu wa Solomo mwana wa Davide unakhala wamphamvu. Yehova Mulungu wake anali naye ndipo anamuchititsa kukhala wamphamvu kwambiri.+
12 ndikupatsa nzeru ndi luso lodziwa zinthu. Ndikupatsanso katundu, chuma ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhaleko ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.