1 Mbiri 21:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Gadi,+ wamasomphenya wa Davide kuti: 10 “Pita, ukamuuze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali zilango zitatu zimene ndingakupatse ndipo iwe usankhepo chimodzi.”’”
9 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Gadi,+ wamasomphenya wa Davide kuti: 10 “Pita, ukamuuze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali zilango zitatu zimene ndingakupatse ndipo iwe usankhepo chimodzi.”’”