2 Mbiri 11:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rehobowamu ankakhala ku Yerusalemu, ndipo anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko la Yuda. 6 Analimbitsanso mizinda ya Betelehemu,+ Etami, Tekowa,+
5 Rehobowamu ankakhala ku Yerusalemu, ndipo anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko la Yuda. 6 Analimbitsanso mizinda ya Betelehemu,+ Etami, Tekowa,+