Oweruza 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsiku limenelo, Debora+ limodzi ndi Baraki+ mwana wa Abinowamu, anaimba nyimbo iyi:+ Oweruza 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Kenako mafumu a Kanani anamenya nkhondo;+Anamenya nkhondo ku Taanaki, pafupi ndi madzi a ku Megido.+ Iwo sanapezepo siliva woti atenge.+
19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Kenako mafumu a Kanani anamenya nkhondo;+Anamenya nkhondo ku Taanaki, pafupi ndi madzi a ku Megido.+ Iwo sanapezepo siliva woti atenge.+