Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova abwezere mʼmalo mwa ine,+ koma dzanja langali silidzakuchitirani choipa.+

  • 1 Samueli 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzaona nkhaniyi nʼkundiweruza kuti ndine wosalakwa+ ndipo adzandipulumutsa mʼmanja mwanu.”

  • 1 Samueli 26:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova ndi amene adzabwezera aliyense mogwirizana ndi chilungamo chake+ komanso kukhulupirika kwake. Lero Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga, koma sindinafune kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+

  • Salimo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.

      Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+

      Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena