Oweruza 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analola mitundu yotsatirayi kukhalabe mʼdzikoli nʼcholinga choti ayese Aisiraeli onse amene anali asanaonepo nkhondo zimene mtunduwo unamenya ku Kanani.+ Oweruza 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu yake inali olamulira 5 a Afilisiti,+ Akanani onse, Asidoni+ komanso Ahivi+ okhala mʼphiri la Lebanoni,+ kuchokera kuphiri la Baala-herimoni mpaka ku Lebo-hamati.*+
3 Yehova analola mitundu yotsatirayi kukhalabe mʼdzikoli nʼcholinga choti ayese Aisiraeli onse amene anali asanaonepo nkhondo zimene mtunduwo unamenya ku Kanani.+
3 Mitundu yake inali olamulira 5 a Afilisiti,+ Akanani onse, Asidoni+ komanso Ahivi+ okhala mʼphiri la Lebanoni,+ kuchokera kuphiri la Baala-herimoni mpaka ku Lebo-hamati.*+