Yoswa 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukachitire mzinda wa Ai ndi mfumu yake zimene unachitira mzinda wa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto zamumzindawo mukatenge zikhale zanu. Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.” Salimo 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye amaphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,Manja anga angathe kukunga uta wakopa.*
2 Ukachitire mzinda wa Ai ndi mfumu yake zimene unachitira mzinda wa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto zamumzindawo mukatenge zikhale zanu. Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.”