Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mudzathamangitsa adani anu ndi kuwagonjetsa ndi lupanga. 8 Anthu anu 5 adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+

  • Deuteronomo 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova adzachititsa adani anu amene adzakuukireni kugonja pamaso panu.+ Pobwera kudzakuukirani adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso panu, adzadutsa njira zosiyanasiyana 7.+

  • 2 Samueli 10:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Yowabu ndi amuna amene anali naye anapita kukamenyana ndi Asiriya ndipo Asiriyawo anayamba kuthawa.+ 14 Aamoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa Abisai nʼkupita mumzinda. Yowabu atamaliza kumenyana ndi Aamoni anabwerera ku Yerusalemu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena