2 Samueli 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhondo imeneyi itatha, panayambikanso nkhondo ina yomenyana ndi Afilisiti+ ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Safi, mbadwa ya Arefai.+ 1 Mbiri 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Asilikali amphamvu a magulu ankhondo anali Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+ 1 Mbiri 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sibekai+ wa ku Husa, Ilai wa ku Ahohi,
18 Nkhondo imeneyi itatha, panayambikanso nkhondo ina yomenyana ndi Afilisiti+ ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Safi, mbadwa ya Arefai.+
26 Asilikali amphamvu a magulu ankhondo anali Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+