Yoswa 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Palibe Aanaki amene anatsala mʼdziko la Aisiraeli, kupatulapo+ amene ankakhala ku Gaza,+ ku Gati+ ndi ku Asidodi.+ 1 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+
22 Palibe Aanaki amene anatsala mʼdziko la Aisiraeli, kupatulapo+ amene ankakhala ku Gaza,+ ku Gati+ ndi ku Asidodi.+
14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+