Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Tinaonakonso Anefili,* ana a Anaki+ omwe ndi mbadwa za Anefili, moti tikadziyerekezera ndi iwowo, ifeyo timangooneka ngati tiziwala. Iwonso ndi mmene amationera.”

  • Deuteronomo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 (Kale mʼdzikoli munkakhala Aemi,+ anthu amphamvu kwambiri ndiponso ochuluka. Iwo anali ataliatali ngati Aanaki.

  • Deuteronomo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ogi mfumu ya ku Basana ndi amene anali womaliza pa Arefai amene anatsala. Chithatha chimene* anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo ndipo mpaka pano chidakali ku Raba wa Aamoni. Mulitali mwake nʼchokwana masentimita 401,* ndipo mulifupi mwake masentimita 178,* potengera muyezo umene unakhazikitsidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena