1 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfilisitiyo anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikunyoza asilikali a Isiraeli+ lero. Ndipatseni munthu woti ndimenyane naye!” 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza ndi kumunyoza?+ Ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+
10 Mfilisitiyo anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikunyoza asilikali a Isiraeli+ lero. Ndipatseni munthu woti ndimenyane naye!”
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza ndi kumunyoza?+ Ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+