Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, mzindawu anaupatsa dzina loti Dani,+ kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani, amene anali mwana wa Isiraeli.+ Koma dzina loyamba la mzindawu linali Laisi.+ 2 Samueli 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malangizo anga ndi akuti: Musonkhanitse Aisiraeli onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Akhale ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo inuyo muwatsogolere kunkhondo.
29 Kuwonjezera apo, mzindawu anaupatsa dzina loti Dani,+ kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani, amene anali mwana wa Isiraeli.+ Koma dzina loyamba la mzindawu linali Laisi.+
11 Malangizo anga ndi akuti: Musonkhanitse Aisiraeli onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Akhale ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo inuyo muwatsogolere kunkhondo.