2 Samueli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yowabu anapereka kwa mfumu chiwerengero cha anthu onse. Aisiraeli anali ndi asilikali 800,000 amphamvu okhala ndi lupanga, ndipo Ayuda anali ndi asilikali 500,000.+
9 Yowabu anapereka kwa mfumu chiwerengero cha anthu onse. Aisiraeli anali ndi asilikali 800,000 amphamvu okhala ndi lupanga, ndipo Ayuda anali ndi asilikali 500,000.+