Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire tchimo langa, ngakhale kuti ndi lalikulu. Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+