2 Mafumu 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+
35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+