Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inuyo ndi amene ndakuchimwirani kwambiri kuposa aliyense.*+Ndachita chinthu chimene mumachiona kuti ndi choipa.+ Choncho mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo,Ndipo mukamaweruza, mumaweruza mwachilungamo.+
4 Inuyo ndi amene ndakuchimwirani kwambiri kuposa aliyense.*+Ndachita chinthu chimene mumachiona kuti ndi choipa.+ Choncho mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo,Ndipo mukamaweruza, mumaweruza mwachilungamo.+