Ekisodo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mukawawonongatu Aiguputo anena kuti, ‘Anali ndi zolinga zoipa powatulutsa mʼdziko lino. Iye amafuna kuti akawaphe kumapiri nʼkuwafafaniza padziko lapansi.’+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo, ndipo sinthani maganizo anu ofuna kubweretsera anthu anu tsoka limeneli. Numeri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, nʼkunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa anthu onse,*+ kodi mukupsera mtima gulu lonseli+ chifukwa cha kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha?”
12 Mukawawonongatu Aiguputo anena kuti, ‘Anali ndi zolinga zoipa powatulutsa mʼdziko lino. Iye amafuna kuti akawaphe kumapiri nʼkuwafafaniza padziko lapansi.’+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo, ndipo sinthani maganizo anu ofuna kubweretsera anthu anu tsoka limeneli.
22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, nʼkunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa anthu onse,*+ kodi mukupsera mtima gulu lonseli+ chifukwa cha kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha?”