Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mfumu inapita ku Gibiyoni kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko nʼkumene kunali malo okwezeka otchuka* kwambiri.+ Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+

  • 1 Mbiri 16:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Zadoki+ wansembe ndi ansembe anzake anawasiya kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibiyoni,+

  • 2 Mbiri 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapita kumalo okwezeka ku Gibiyoni.+ Anapita kumeneko chifukwa nʼkumene kunali chihema chokumanako cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki wa Yehova anapanga mʼchipululu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena