-
1 Mbiri 26:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Maere akumʼmawa anagwera Selemiya. Anachitanso maere a Zekariya mwana wake, yemwe anali mlangizi wanzeru ndipo maere ake anasonyeza kuti akakhale kumpoto.
-
-
1 Mbiri 26:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Amenewa anali magulu a alonda apageti ochokera ku mbadwa za Kora ndi za Merari.
-