-
1 Mbiri 29:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho akalonga a nyumba za makolo, akalonga a mafuko a Aisiraeli, atsogoleri a magulu a anthu 1,000 ndi a magulu a anthu 100+ ndiponso atsogoleri oyangʼanira ntchito za mfumu,+ anabwera nʼkuyamba kupereka zinthu mwa kufuna kwawo. 7 Iwo anapereka golide wokwana matalente 5,000, madariki* 10,000, siliva wokwana matalente 10,000, kopa wokwana matalente 18,000 ndi zitsulo zokwana matalente 100,000. Anapereka zonsezi kuti zigwire ntchito panyumba ya Mulungu woona.
-