Deuteronomo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzipita kwa Alevi omwe ndi ansembe ndi kwa woweruza+ amene akutumikira mʼmasiku amenewo. Muziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuzani chigamulo.+ 2 Mbiri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena, ansembe ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo a Isiraeli, kuti akhale oweruza mʼmalo mwa Yehova ndipo aziweruza milandu ya anthu a ku Yerusalemu.+
9 Muzipita kwa Alevi omwe ndi ansembe ndi kwa woweruza+ amene akutumikira mʼmasiku amenewo. Muziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuzani chigamulo.+
8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena, ansembe ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo a Isiraeli, kuti akhale oweruza mʼmalo mwa Yehova ndipo aziweruza milandu ya anthu a ku Yerusalemu.+