Yoswa 13:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso Mose anagawira cholowa fuko la Gadi motsatira mabanja awo. 25 Dera lawo linali mzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi komanso hafu ya dziko la Aamoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli kufupi ndi Raba.+ Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
24 Komanso Mose anagawira cholowa fuko la Gadi motsatira mabanja awo. 25 Dera lawo linali mzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi komanso hafu ya dziko la Aamoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli kufupi ndi Raba.+
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.