1 Mbiri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Otsatirawa ndi amene anali asilikali amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 nthawi imodzi.+
11 Otsatirawa ndi amene anali asilikali amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 nthawi imodzi.+