2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi. 2 Samueli 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abi-ezeri+ wa ku Anatoti,+ Mebunai wa ku Husa,*
8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi.