1 Samueli 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli. 2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+
50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli.
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+