2 Samueli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ mchimwene wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wochenjera kwambiri. 2 Samueli 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ankanyoza kwambiri Aisiraeli.+ Choncho Yonatani mwana wa Simeyi,+ mchimwene wake wa Davide, anamupha.
3 Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ mchimwene wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wochenjera kwambiri.
21 Iye ankanyoza kwambiri Aisiraeli.+ Choncho Yonatani mwana wa Simeyi,+ mchimwene wake wa Davide, anamupha.