-
2 Samueli 16:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Husai+ mbadwa ya Areki,+ mnzake wa Davide, atafika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!” 17 Zitatero Abisalomu anafunsa Husai kuti: “Kodi zimene wachitazi wamusonyeza mnzako chikondi chokhulupirika? Nʼchifukwa chiyani sunapite naye limodzi mnzakoyo?”
-