1 Mafumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwandiika ine mtumiki wanu kukhala mfumu mʼmalo mwa Davide bambo anga, ngakhale kuti ndine wamngʼono ndipo sindikudziwa zambiri.+
7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwandiika ine mtumiki wanu kukhala mfumu mʼmalo mwa Davide bambo anga, ngakhale kuti ndine wamngʼono ndipo sindikudziwa zambiri.+