1 Mbiri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso Davide anasonkhanitsa zitsulo zambirimbiri zopangira misomali ya zitseko za mageti ndiponso zopangira zida zopanira zinthu. Anasonkhanitsanso kopa* wambirimbiri wosatheka kumuyeza kulemera kwake.+ 1 Mbiri 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Golide, siliva, kopa ndi zitsulo nʼzosatheka kuziwerenga.+ Yamba kugwira ntchito imeneyi ndipo Yehova akhale nawe.”+
3 Komanso Davide anasonkhanitsa zitsulo zambirimbiri zopangira misomali ya zitseko za mageti ndiponso zopangira zida zopanira zinthu. Anasonkhanitsanso kopa* wambirimbiri wosatheka kumuyeza kulemera kwake.+
16 Golide, siliva, kopa ndi zitsulo nʼzosatheka kuziwerenga.+ Yamba kugwira ntchito imeneyi ndipo Yehova akhale nawe.”+