-
1 Mbiri 22:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndayesetsa mwakhama kusonkhanitsa golide womangira nyumba ya Yehova wokwana matalente* 100,000 ndi siliva wokwana matalente 1 miliyoni. Koma nʼzosatheka kuyeza kulemera kwa kopa ndi zitsulo+ chifukwa nʼzochuluka kwambiri. Ndasonkhanitsanso matabwa ndi miyala+ pokonzekera, koma udzawonjezerapo zina.
-