Salimo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, ndimakonda nyumba imene inu mumakhala,+Malo amene kumakhala ulemerero wanu.+ Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+ Salimo 122:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 122 Ndinasangalala pamene anandiuza kuti: “Tiyeni tipite kunyumba ya Yehova.”+
4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+