Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 22:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yosiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 8 ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya. 2 Yosiya anachita zoyenera pamaso pa Yehova ndipo anayenda mʼnjira zonse za Davide kholo lake.+ Iye sanapatukire kumanja kapena kumanzere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena