2 Mafumu 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mfumuyo inatulutsa mzati* wopatulika+ umene unali mʼnyumba ya Yehova ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu nʼkukautentha.+ Itatero, inauperapera nʼkuwaza fumbi lake pamanda a anthu wamba.+
6 Mfumuyo inatulutsa mzati* wopatulika+ umene unali mʼnyumba ya Yehova ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu nʼkukautentha.+ Itatero, inauperapera nʼkuwaza fumbi lake pamanda a anthu wamba.+