Levitiko 26:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Amenewa ndi malangizo, zigamulo komanso malamulo amene Yehova anakhazikitsa pakati pa iye ndi Aisiraeli mʼphiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+
46 Amenewa ndi malangizo, zigamulo komanso malamulo amene Yehova anakhazikitsa pakati pa iye ndi Aisiraeli mʼphiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+