2 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali Hefiziba. 2 Mafumu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anachotsa.+ Komanso anamanga maguwa ansembe a Baala ndi mzati wopatulika,*+ ngati mmene Ahabu mfumu ya Isiraeli anachitira.+ Manase ankalambira ndiponso kutumikira gulu lonse la zinthu zakuthambo.+ 2 Mafumu 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto, ankachita zamatsenga, ankawombeza+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu komanso olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa. 2 Mbiri 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+ 2 Mbiri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.
21 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali Hefiziba.
3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anachotsa.+ Komanso anamanga maguwa ansembe a Baala ndi mzati wopatulika,*+ ngati mmene Ahabu mfumu ya Isiraeli anachitira.+ Manase ankalambira ndiponso kutumikira gulu lonse la zinthu zakuthambo.+
6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto, ankachita zamatsenga, ankawombeza+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu komanso olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.
28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+
3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.