2 Mbiri 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumuyo itangomva mawu a Chilamulowo, inangʼamba zovala zake.+