38 Ndipo mʼchaka cha 11, mwezi wa Buli,* (womwe ndi mwezi wa 8), anamaliza zinthu zonse panyumbayo mogwirizana ndi pulani yake.+ Choncho Solomo anamanga nyumbayo zaka 7.
7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova pamalo ake, kuchipinda chamkati cha nyumbayo, chomwe ndi Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+