1 Mbiri 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la pangano la Yehova, kuti azitumikira nthawi zonse kumene Likasalo linkakhala,+ mogwirizana ndi zofunika kuchita pa tsikulo.+
37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la pangano la Yehova, kuti azitumikira nthawi zonse kumene Likasalo linkakhala,+ mogwirizana ndi zofunika kuchita pa tsikulo.+